Chipani cha UTM chadzudzula nthambi zachitetezo ati kamba kolephela kumanga anthu amene amapanga zachiwembuzo. Chipanichi chadzudzulanso mchitidwe wa zipolowe omwe anthu ena anachitira otsatira chipani cha DPP dzulo ku Lilongwe. Kudzela mu kalata yomwe wasainira ndi mneneri wake Felix Njawala, UTM yati ndale zomaophyezana ndizachikale komanso zilibe malo mu ulamuliro wa demokalase. Chipani cha UTM […]
The post Chipani cha UTM chidzudzula a polisi polephera kumanga anthu anayambisa ziwembu ku Lilongwe appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.