Chipani cha UTM chati chakonza mwambo oyatsa kandulo kufupi ndi malo amene ndege imene anakwera Saulosi Chilima inagwera ku Mzimba mmawa lino. Mlembi wamkulu wachipinichi, Patricia Kaliyati wauza Nyasatimes kuti mwambowu ndi mbali imodzi ya zochitika zimene chipani chawo chakonza pofuna kukumbukira mtsogoleri wawo. Chihaula Shaba, m’modzi mwa akuluakulu a chipani cha UTM mchigawo […]
The post Chipani cha UTM chatsimikiza kuti chikukapanga mwambo woyatsa makandulo pamalo pomwe ndege inagwera appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.