Chipani cha PP chati chiziwa za tsogolo lake mu Tonse Alliance kumapeto kwa chaka chino

Chipani cha People’s (PP) chati tsogolo pa mgwirizano wake ndi zipani zina pansi pa mgwirizano wa Tonse udziwika kumapeto a chaka chino pamene chipanichi chikhale chikuchititsa msonkhano wake waukulu pa 7 September mu mzinda wa Lilongwe. Wofalitsa nkhani za chipanichi a Ackson Kalaile Banda wati nthumwi za chipanichi zokwana 400 ndi zomwe zidzakambirane ndi kugwirizana […]

The post Chipani cha PP chati chiziwa za tsogolo lake mu Tonse Alliance kumapeto kwa chaka chino appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください