Chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) chati Peter Mutharika ndiye yankho la a Malawi ndipo ngati mtsogoleri wachipanichi ndiwokonzeka kudzapikisana nawo pachisankho cha 2025. Gavanala wachipani cha DPP mchigawo chakum’mawa a Imran Ntenje ndi womwe ayankhula izi pomwe chipanichi chidakonza misonkhano yoyimaima yomwe akuyitchula kuti Blue Convoy mu boma la Zomba. A Ntenje adati malo […]
The post Chipani cha DPP chati Mutharika ndiye yankho la a Malawi appeared first on Malawi 24.