Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe yati yatchetcha minda Khumi (10) ya chimanga chifukwa cholima mbewuzi m’malo oletsedwa. Khonsoloyi kudzela ku mbali yokhwimitsa lamulo ati dongosolo lotchetcha chimanga ndi mbewu zina zomwe anthu analima m’malo osaloledwa likhala likupitilira. Malingana ndi wamkulu wa okhwimitsa malamulo mu khonsoloyi a Allan Domingo ati ayamba ndi madela a ku 43 […]
The post Chimanga chovuta kale a Khonsolo achitchetcha cha nthete appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 