Chilima sanaletsedwe kuyendera anthu – Kunkuyu

A boma atsutsa mphekesera zomwe zikumveka zoti wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima analetsedwa kutulukira a Malawi amene akhudzidwa ndi mphepo ya namondwe ya Freddy. A Malawi ambiri akhala akudabwa kuti mtsogoleri wa chipani cha UTM amenenso ali wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko a Saulos Chilima ndi wa ndale ekhayo amene wabindikira. […]

The post Chilima sanaletsedwe kuyendera anthu – Kunkuyu appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください