Chilima: Munthu wanzeru saotcha tchire nyumba ilibe chimbudzi

Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima ati munthu wa nzeru saotcha tchire lozungulira nyumba ngati nyumbayo ilibe chimbudzi. Iwo ananena izi dzulo ku Kamuzu International Airport poyankhula ndi owatsatira pomwe amafika mdziko muno kuchokera ku United States of America. Iwo anapereka miyambi iwiri ndipo oyamba ndi okuti okazinga soya sadikira mbuliuli pomwe […]

The post Chilima: Munthu wanzeru saotcha tchire nyumba ilibe chimbudzi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です