Wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, Dr Saulosi Klaus Chilima, akuyembekezeka kudzakhala nawo pa mkumano omwe wakonzedwa ndi ophunzira a Bungwe la Katorika ku Sukulu ya Ukachenjede ya Malawi ku Zomba pa 4 May chaka chino yomwe idzachitike ndi mutu okuti “Call for Evangelisation.” Wapampando wa Bungweli, Wisdom Sauka, wauzza Malawi24 kuti zochitika patsikuli zidzayamba ndi […]
The post Chilima akakhala nawo pa mkumano wa ophunzira a Chikatolika ku Sukulu ya Ukachenjede ya Malawi appeared first on Malawi 24.