Chikhulupiliro cha Habakkuk n’chosuntha phiri

Patangodutsa sabata imodzi pomwe Prophet Shepherd Bushiri adapeleka ndalama zokwana 6 miliyoni kwacha kwa ‘M’neneri’ Habakkuk kutsatira pempho lomwe adapereka, lero Habakkuk wapemphanso thandizo lina kwa m’neneli Bushiri. Mneneri Habakuk ati akufuna thandizo loti amangire nyumba ya zonse mom’mo ya zipinda zokwana 8 komanso thandizo lomangira ma boyizikota okwana 10 kapena 7 okhala ndi zipinda […]

The post Chikhulupiliro cha Habakkuk n’chosuntha phiri appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください