Pomwe masiku akusendera ku chitseko kuti dziko lino lichititse chisankho chaka cha mawa, mlembi wa chipani cha UTM a Patricia Kaliati ati ndiothokoza kuti chikhulupiliro cha anthu ochuluka mdziko muno chili mwa chipani chawo koma ati afotokozabe posachedwapa ngati chipanichi chipitilire kukhalabe mu mgwirizano wa Tonse kapena ayi. A Kaliati ayankhula izi pomwe amacheza ndi […]
The post Chikhulupiliro cha anthu chili mwa UTM – atelo a Kaliati appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
