Mfumu ina yazaka 40 ku Lilongwe yalamulidwa kukaseweza jere kwa zaka 20 itapezeka yolakwa pa mlandu oti idagwilira mwana wazaka 13 m’munda wachimanga pamene mwanayo amkatchola nkhwani atatumidwa ndi amake. Malingana ndi mneneri wa apolisi m’bomali a Hastings Chigalu ati mfumuyi yomwe dzina lake ndi a Pitilosi Khote, adachita zadamazi ndi mwanayu m’mwezi wa June […]
The post Chepetsaniko zakazo ndimadwala nthenda ya shuga, inatero mfumu yogwilirayo appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
