Mkulu woyang’anila bungwe loona za mphamvu la MERA, a Henry Kachaje auza a Malawi kuti asiye kaye zoyendayenda ndi cholinga chofuna kupulumutsa mafuta a galimoto. Polankhula pa msonkhano wa atolankhani umene bungwe lawo lachititsa mu boma la Lilongwe, a Kachaje anati kupezeka kwa mafuta kukuyenela kulongosoka pofika lachitatu sabata la mawa. “Tikunena pano, ma thankala […]
The post Chepetsani kuyendayenda – Kachaje auza a Malawi pamene a Matola ati mafuta sanavute kwenikweni appeared first on Malawi 24.