Bungwe loona za chilungamo pamalonda la CFTC lati lalandila uthenga kuchoka ku kampani ya Loreal South Africa kuti yayamba kuitanitsa mankhwala otsukira tsitsi a Loreal Dark and Lovely Anti Breakage Kit komanso Mosture Plus Kit (Regular and Super) kamba koti ali ndi chiopsezo kuumoyo wa athu. Mneneri kubungwe la CFTC an Innocent Herema wati kampaniyi […]
The post Chenjerani! Loreal Dark and Lovely ndiwoyipa, ali ndi chiopsezo pa moyo wanu, boma latero appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.