Chipani cha Democratic Progressive Party (DPP), chasankha a George Chaponda kukhala mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma m’nyumba ya malamulo, kulowa m’malo mwa a Kondwani Nankhumwa omwe adawachotsa m’chipanichi ndipo a tula pansi udindowu sabata latha. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe chipanichi chaatulutsa Lachiwiri pa 7 May, 2024 yomwe wasainira ndi Shadric Namalomba yemwe ndi […]
The post Chaponda walowa m’malo mwa Nankhumwa appeared first on Malawi 24.