Matani a chamba olemera makilogalamu oposa 1,150 omwe analandidwa kwa anthu osiyanasiyana chaka chino athilidwa moto ndi apolisi ku Mponela m’boma la Dowa dzulo. Malingana ndi mneneri wa apolisi m’bomali a Macpstson Msadala, apolisi atentha chambachi chomwe njonda zina zinkafuna kuzembetsa kanunduyu. Kutenthedwa kwa katunduyu ndi malingana ndi ndondomeko zomwe adakhazikitsa kuti chambachi achithire moto […]
The post Chamba chathilidwa moto ndi apolisi appeared first on Malawi 24.