Ntchito yogawa chimanga ku mabanja omwe akhudzidwa ndi njala m’boma la Mulanje yayamba lero, lolemba kwa Mthiramanja komwe mabanja 1200 alandira chimangachi. DC wa boma la Mulanje a David Kayiwonanga Gondwe ati mabanja 69,497 ndiwo alandire chimanga m’boma lonse la Mulanje kwa miyezi isanu m’bomali. A Gondwe apempha anthu kuti apewe chisokonezo ndi ziwawa pa […]
The post Chakwera wayamba kugawa chakudya kwa a Malawi osowa: Mabanja 1200 athandizidwa ku Mulanje appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.