Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera watsimikizira nzika za dziko lino kuti boma lake lakangalika pa ntchito yotuluka luso la makono ngati njira imodzi yotukulira maphunziro mdziko muno. Achakwera adati ndi cholinga chawo kuona ana akugwiritsa ntchito makina a computer komanso ma lamya akulu akulu a tabuleti. Polankhula pa msonkhano wa chitukuko omwe anachititsa […]
The post Chakwera watsindika zakufunika kwa luso la makono ngati njira imodzi yotukulira maphunziro appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.
Moni Malawi 
