Mtsogoleri wa dziko lino Dr. Lazarus McCarthy Chakwera watsimikizira aMalawi ndi mayiko onse akunja kuti boma lake liwonetsetsa kuti ngozi ya ndege ifufuzidwa mosabisa komanso mwapadera pofuna kuti chilungamo chidziwike. Chakwera wanena izi pa Bingu National Stadium mu mzinda wa Lilongwe pa mwambo wokhudza maliro a yemwe anali wachiwiri wake, Dr. Saulos Klaus Chilima. Chilima […]
The post Chakwera watsimikizira aMalawi kuti ngozi ya ndege ifufuzidwa mosabisa komanso mwapadera appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.