Chakwera wapeleka puloti, K1.5 miliyoni kwa osewera aliyese wa Scorchers

Asungwana osewera mpira wa miyendo mu timu ya dziko lino ya Scorchers, akusimba lokoma pomwe mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati apereka 1.5 million kwacha komanso malo omangapo nyumba kwa osewera aliyese. Chakwera walengeza za nkhaniyi lero lachitatu ku nyumba ya boma ya Kamuzu munzinda Lilongwe komwe anakonzera nkhomaliro osewera atimu ya Scorchers pokondwelera […]

The post Chakwera wapeleka puloti, K1.5 miliyoni kwa osewera aliyese wa Scorchers appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください