Chakwera wanenetsa kuti sakutuluka m’boma chaka cha mawa

Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati wina asamanamize anthu m’dziko muno kuti iwo atuluka m’boma chaka cha mawa. Mtsogoleriyu, poyankhula pa mwambo wokumbukira mtsogoleri wakale wadziko lino Hastings Kamuzu Banda, anati boma lake lipitiliza kupanga zitukuko m’zigawo zonse za dziko lino chifukwa alibe nthawi yolimbana ndi anthu ena. “Olo anthu okonda ndale za miseche […]

The post Chakwera wanenetsa kuti sakutuluka m’boma chaka cha mawa appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください