Anthu m’boma la Lilongwe anaiwala kuti mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera anali pa chisoni pomwe anamukuwiza kuti “tipatse mafuta” nthawi yomwe amachokera ku mwambo oyika m’manda malemu John Tembo. Lachitatu pa 4 October, 2023, a Chakwera anali m’mudzi mwa Kaphala mfumu yaikulu Kaphuka m’boma la Dedza komwe thupi la mtsogoleri wakale wa chipani cha […]
The post Chakwera wakuwizidwa appeared first on Malawi 24.