Mtsogoleri wa dziko la Dr. Lazarus McCarthy Chakwera Lachinayi madzulo adakumana ndi kukambirana ndi ochita malonda ochokera ku chigawo chakumvuma cha dziko pofuna kulimbikitsa ubale ndi umodzi potukula Malawi. Mkumanowo udachitikira ku nyumba ya boma ya Chikoko Bay State Lodge ndipo udayitanitsidwa ndi cholinga chowapatsa mavendawa mwayi wokumana ndi mtsogoleri wa dziko. Polankhula pa mkumanowo, […]
The post Chakwera, mavenda achigawo chakumvuma agwirizana zogwira ntchito limodzi potukula Malawi appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.