Iyi ithera ku waya ndithu. Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera akuoneka kuti sanathane ndi moto omwe owatsutsa a Peter Mutharika adayatsa ku Blantyre lamulungu lapitali pa msonkhano wawo wandale. Adakapitiriza kuwayankha mokuluwika. Lero lachinayi a Chakwera adzudzula atsogoleri omwe akupitiriza kuwanena kuti ndiolephera. Iwo anena izi mu mzinda wa Lilongwe. A Chakwera ati […]
The post Chakwera ayankhanso Mutharika: ulamuliro wanga wakumana ndi zokhoma zambiri ndi chifukwa ndalephera appeared first on Malawi 24.