Mtsogoleri wadziko lino Dr Lazarus Chakwera lero wakumana ndi mlembi wamkulu wa bungwe la International Federation of Red Cross (IFRC) kuno ku Malawi a Jagannath Chapagain yemwe wangosankhidwa kumene. Mmawu ake a Chakwera ayamikira bungwe la International Federation of Red Cross chifukwa cha thandizo lomwe bungweli limapereka kudziko la Malawi. A Chakwera anathokoza bungweli maka […]
The post Chakwera ayamikila Bungwe la Red Cross kamba ka ntchito zabwino zomwe bungweli lakhala likupanga appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.