Chakwera awowozedwa ku Lilongwe

Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera awowozedwa ku Lilongwe pomwe amadutsa pa malo othilira mafuta a galimoto. A Chakwera anali pa mdipiti wa galimoto pomwe anadutsa pa malo ena ogulitsira mafuta lero. Pamalowa panali gulu la anthu lomwe limadikira kuti lipeze mwayi ogula mafuta omwe pakali pano akusowa. Pomwe a Chakwera amadutsa, anthu anayamba […]

The post Chakwera awowozedwa ku Lilongwe appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください