Chakwera atukwanidwa ku Blantyre

Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera lolemba sabata ino anawowozedwa komaso kutukwanidwa ndi anthu mumzinda wa Blantyre. Izi ndimalinga ndi kanema yemwe tsamba lino lawona yemwenso anthu akugawana m’masamba a mchezo yemwe akuonetsa anthu akutukwana mtsogoleri wa dzikoyu pomwe amachoka kokagwira ntchito ya boma ku Thyolo. Patsikuli a Chakwera anapita kokayendera mbewu m’minda mwa anthu […]

The post Chakwera atukwanidwa ku Blantyre appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です