Chakwera athandiza anthu omwe akhudzidwa ndi ngozi yodza kamba kosefukira kwa madzi

Tate wa pfuko la Malawi , Dr Lazarus McCarthy Chakwera lero wapereka katundu osiyana siyana kwa anthu omwe akubvutika ndi madzi osefuka mboma la Karonga. Chakwera wapereka ufa , ziwiya zophikira , ndiwo ndi katundu winanso kwa ndi cholunga choti anthu kumeneko athandizike mdelaro. Poyankhula atayendera misasa ya Kambwe ku Karonga, komweko , mtsogoleri wa […]

The post Chakwera athandiza anthu omwe akhudzidwa ndi ngozi yodza kamba kosefukira kwa madzi appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください