Chakwera asiya Malawi pamoto wa ku Iguputo

Ulendo wa ku Kanani walephereka. Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wasiya Malawi akulira ndikuphula njerwa za moto. Chakwera  yemwe anayenda mwakachetechete kuopa kuwowozedwanso ku Lilongwe akuti wafika bwino ku Iguputo. Lachisanu, a Chakwera anawowozedwa pamene amadutsa pa malo othilira mafuta pomwe gulu la a anthu linaunjikana kudikira kugula mafuta. Dzulo popita ku Iguputo a […]

The post Chakwera asiya Malawi pamoto wa ku Iguputo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください