Boma lati mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera ayenda ndi anthu osachepera 70 paulendo wake opita ku mayiko a Saudi Arabia komanso Egypt womwe anyamuke mawa lachitatu. Malingana ndi nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu, a Chakwera akuyembekezeka kukakhala nawo pa chiwonetsero cha malonda chomwe chikutchedwa Egypt Intra-Africa Trade Fair. A Kunkuyu ati ku Saudi […]
The post Chakwera apita ku Saudi Arabia ndi Egypt ndi anthu osachepera 70 appeared first on Malawi 24.