Mtsogoleri wadziko lino a LazarusChakwera yemwenso ndi wamkulu kunthambi ya a polisi, wapempha apolisi mdziko muno kuti akhale anthu osunga mwambo. Mukulankhula kwawo ku mwambo otsanzikana ndi ophunzira ku sukulu zanthambiyi, ku Blantyre, a Chakwera adati zimakhala zomvetsa chisoni kuona a Polisi kukhalanso oyamba kumphwanya malamulo. A Chakwera adati a Polisi ndi anthu ofunika kwambiri […]
The post Chakwera apempha apolisi kuti akhale osunga mwambo appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.