Akuluakulu aboma ati ngakhale msonkhano omwe umayenera kuchitika m’dziko la Saudi Arabia walepheleka, mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera anyamukabe lero masanawa kupita m’dzikolo. Lachiwiri sabata ino boma linalengeza kuti a Chakwera anyamuka lero Lachitatu kupita m’dziko la Saudi Arabia komwe akakhale nawo pa nkumano wa mayiko a mu Africa komaso maiko anchigawo cha […]
The post Chakwera anyamukabe lero ngakhale msonkhano waku Saudi Arabia walepheleka appeared first on Malawi 24.