Chakwera alunjika ku USA

Patangopita masiku ochepa chipitireni m’dziko la Kenya, mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera akuyembekezera kupita m’dziko la United States of America Lachisano likudzali. Malingana ndi kalata yomwe unduna owona za ubale wa dziko lino ndi mayiko akunja watulutsa, a Chakwera akuyenera kukakhala nawo pa msonkhano wa zamalonda pakati pa America ndi Africa ku Dallas, Texas, […]

The post Chakwera alunjika ku USA appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください