Nduna yowona za maboma ang’ono a Richard Chimwendo Banda ati amene akulota kuti alowanso m’boma apitilize kulota kamba koti m’tsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera alamulira mpaka 2030. Ndunayi yayankhula izi pa chikondwelero chokumbukira mtsogoleri oyamba wadziko lino Malemu Ngwazi Dr. Hastings Kamuzu Banda ku Blantyre pa Kamuzu Stadium. A Chimwendo anati Kamuzu anali […]
The post Chakwera alamulira 2030 woo, atero a Chimwendo-Banda appeared first on Malawi 24.