Chakwera akutsekulira nsika wa fodya

Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera, lero ali m’boma la Kasungu komwe watsegulira nyumba ya Tobacco Commission yomwe yamangidwa posachedwapa komanso akuyembekezeka kutsekulira nsika wa fodya ndi kuyendera nyumba za asilikali zomwe zikumangidwa.  Izi ndi malingana ndi kalata yomwe boma latulutsa yomwe yasainilidwa ndi mlembi wankulu mu ofesi yamtsogoleri wa dziko lino ndi nduna a […]

The post Chakwera akutsekulira nsika wa fodya appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください