Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera mawa lachisanu akhala ali m’boma la Dowa komwe akawonelere kukolora koyamba kwa Tirigu pa munda wina kenaka akukakhazikitsa ndondomeko ya fetereza wotchipa ku Kasungu. Izi ndi malingana chikalata chomwe boma latulutsa chomwe wasayinira ndi mlembi wa mkulu wa boma mayi Colleen Zamba. Mayi Zamba munkalatayi ati mtsogoleri wadzikoyu akakhala […]
The post Chakwera akawonelera kukolora tirigu ku Dowa appeared first on Malawi 24.