Chakwera adzudzula boma la USA poletsa a Malawi ena kupita ku USA: ‘Akuzengedwa milandu, khoti silidawapezebe olakwa.’

President Lazarus Chakwera wati ndiodabwa ndi ganizo la dziko la America loletsa mzika zinayi zadzikolino kupita mdzikoli ati kamba kokhudzidwa ndi mchitidwe wa ziphuphu ndi katangale. Mtsogoleriyu wati ndizodabwitsa kuti dziko la America likupeleka chilango kwa anthu omwe bwalo lamilandu kuno silidawapeze olakwa chikhalirecho ku America ko kumachitika umbava ndi umbanda ochuluka kuposa ku Malawi […]

The post Chakwera adzudzula boma la USA poletsa a Malawi ena kupita ku USA: ‘Akuzengedwa milandu, khoti silidawapezebe olakwa.’ appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください