Chakwera aboola mtambo lero wa ku DRC

Mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera akuyembekezeka kuboola mtambo lero pa ulendo opita mdziko la Democratic Republic of Congo (DRC). A Chakwera akukawonelera mwambo olumbilitsa mtsogoleri wadzikolo a Felix Tshisekedi Tshilombo yemwe wangosankhidwanso  kumene komanso akukakambilana ndi a Tshisekedi zokhudzana ndi asilikali a Malawi omwe akugwira ntchito yosungitsa bata ku DRC. Malingana ndi kalata yomwe […]

The post Chakwera aboola mtambo lero wa ku DRC appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください