Kusowa kwa chokudya komanso kuthima kwa magetsi kwasokonedza maphunziro pa sukulu ya secondary ya Mulunguzi Boma la Zomba. M’phunzitsi wankulu wapasukuluyi a Silk Kadwala atsimikidza zankhaniyi ndipo ati pakali pano ana akuwalembetsa mayeso pofuna kuti pofika Lachisanu sabata ino ophunzirawa akhale atachoka pasukuluyi chifukwa zinthu zafika poyipa kwambiri. A Kadwala ati magetsi adathima Lamulungu ndipo […]
The post Chakudya komanso magetsi zavuta pa sukulu ya Mulunguzi appeared first on Malawi 24.