Chakudya chavuta mu ndende za mdziko lino pomwe akaidi akungodya nyemba zokha kapena phala chifukwa cha kukwera kwa mitengo kwa zinthu m’dziko. Ndizachidziwikire kuti kudya kwa kundende kumakhala kosiyaniranatu ndi mmene anthu ena omwe sali mndende amadyera, koma vutoli lafika pamwana wakana phala pomwe pano akaidi akumangodya nyemba zophika komanso phala. Izi zadza kamba kakuti […]
The post Chakudya chavuta mu ndende za mdziko lino appeared first on Malawi 24.