“Osewera tagwirizana kutenga zikho zonse,” mhuuu! Anakadziwa sanakayankhula, maloto a chumba enieni, chimanjamanja ikutuluka m’chakachi. Tsoka la mfutso lopita pa moto kawiri ndipo kupsa kwake ndi kwa chigumu, pansi ndi pa mwamba. Mukutipheranji? Walira movetsa chisoni neba. Khilisimisi yalephereka ku Lali Lubani. Osewera a timu ya Mighty Mukuru Wanderers atagwirizana ku mayambiliro a chakachi kuti […]
The post Chaka chopanda dipo! Mzungu wayinyumwa appeared first on Malawi 24.