Boma kudzera ku bungwe losunga chakudya la National Food Reserve Agency (NFRA) lati lili ndi chimanga chochepa mu nkhokwe zake, zomwe zikupeleka chiopsezo kuti njala ivuta chaka chino. Malingana ndi mkulu wa bodi yoyang’anira bungweli a Dennis Kalekeni, nkhokwe za bungweli zimayenera kukhala ndi chimanga chokwana matani 217,000 koma pano kuli matani 30,000 okha. Iwo […]
The post Chaka chino kuli njala, laopseza motero boma appeared first on Malawi 24.