CDEDI yati ana asabaidwe katemera wa Korona popanda chilolezo cha makolo

Bungwe la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI) lachenjeza aphunzitsi onse komanso ogwira ntchito za umoyo kuti apewe kunyengelera ana asukulu kuti abayitse katemera wa Korona popanda chilolezo cha makolo. Bungweli lanena izi muchikalata chake chomwe lalemba lero ndipo wasainira ndi Mkulu wa bungweli Sylvester Namiwa. A Namiwa apempha ogwira ntchito za umoyo […]

The post CDEDI yati ana asabaidwe katemera wa Korona popanda chilolezo cha makolo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です