CDC Investment yabanduka ndi ndalama za gulu

Anthu omwe amasunga ndalama pa kampani ya pa intaneti ndicholinga chofuna kupeza phindu phwamwamwa, manja ali ku nkhongo kwinaku akudziguguda pa mtima kuti ndinkaganiza chiyani ine pomwe zikumveka kuti kampani ya CDC Inves yabowola mtambo ndi ndalama za gulu za nkhani-nkhani. Mphekesera zikusonyeza kuti kampani ya Cryptopro yomwe imatchukaso ndi dzina loti CDC Investment yawulutsa […]

The post CDC Investment yabanduka ndi ndalama za gulu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください