CCAP yapepesa alhomwe, akhilisitu ake ponyazitsidwa ndi abusa awiri

Akuluakulu a Sinodi kulankhula ndi atolankani Sinodi ya Blantyre mu mpingo wa CCAP, yapepesa kwa anthu amtundu wachi lhomwe komanso a khilisitu ake kaamba kosambulidwa ndi abusa awiri omwe sakumwerana madzi atasemphana chichewa. Mkati mwa sabatayi, tsamba lino linaulutsa nkhani yoti abusa awiri a sinodiyi apindirana ndevu mkamwa potsatira chisankho cha adindo chomwe sinodiyi ikuyembekezeka […]

The post CCAP yapepesa alhomwe, akhilisitu ake ponyazitsidwa ndi abusa awiri appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください