Tsopano Mavuto Phiri ndi mfulu popeza bwalo la milandu ku Karonga lathetsa mlandu womwe wakhala akuganizilidwa kuti adapha mchimwene wake mchaka cha 2018 pa mkangano omwe udabuka pakati pa abambo ake ndi mchimwene wake amene amaganizira kuti abambo akewo adali kuchita ubwenzi wanseli ndi mkazi wake. Nkhani yonse ikuti m’mwezi wa September mchaka cha 2018, […]
The post Bwalo lamilandu lamasula njonda ina pa mlandu wakupha appeared first on Malawi 24.