Bwalo la Principal Resident Magistrate ku Zomba likuyembekezeka kudzapereka chigamulo chake pa 10 May kwa mkulu wa Bungwe la Malawi First a Bon Kalindo pamulandu womwe akumuyimba woyambitsa chisokonezo paziwonetsero zomwe adachititsa mu mzinda wa Zomba pa 23 November chaka chatha. A Kalindo adabweretsa mboni zisanu ndipo mboni ziwiri zatsiliza kuperekera umboni wao Lolemba mamawa […]
The post Bwalo lamilandu ku Zomba lidzapereka chigamulo chake pa 10 May pa mulandu wa Bon Kalindo appeared first on Malawi 24.