Bwalo la milandu ku Zomba lapeza olakwa bambo ofuna kugulitsa mwana omupeza

Bwalo la milandu ku Zomba lapeza olakwa bambo wina Chimwemwe Zololo yemwe amafuna kugulitsa mwana omupeza kwa bambo wina ochita malonda ndipo lati lidzapereka chigamulo chake pa 14 February. Wa Police oyimila Boma pa milandu Assistant Superintendent Peter Njiragoma adabweretsa mboni zitatu ndipo yemwe adayamba kuperekera umboni ndi Marita James yemwe ndi mkazi wake wa […]

The post Bwalo la milandu ku Zomba lapeza olakwa bambo ofuna kugulitsa mwana omupeza appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください