Bushiri watulukira! Agawa chimanga kwa anthu opitilira 1 million, chokwana K17 billion

Mtsogoleri wa  mpingo wa Enlightened Christian Gathering International Prophet Shepherd Bushiri walengeza kuti ayambiranso kugawa chakudya kwa anthu opitilira 1 miliyoni omwe akhudzidwa ndi njala mdziko muno. Malinga ndi mneneri Bushiri, ndondomekoyi ipulumutsa Amalawi mamiliyoni ambiri omwe akhudzidwa ndi njala pazifukwa zosiyanasiyana monga Cyclone Freddy. Bushiri wapempha mabungwe akuluakulu aboma ndi anthu onse kuti awonetsetse […]

The post Bushiri watulukira! Agawa chimanga kwa anthu opitilira 1 million, chokwana K17 billion appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください