Mneneri Shepherd Bushiri kudzera pansi pa bungwe la Shepherd Bushiri Foundation (SBF) wasainirana mgwirizano ndi katakwe pa nkhani yochita ma filimu wa m’dziko la Nigeria, Nkem Owoh, lamulungu lapitali mu mzinda wa Lilongwe ngati njira imodzi yopititsa patsogolo luso lochita mafilimu m’dziko muno. Uthenga omwe walemba ndi oyankhulira a Bushiri, Aubrey Kusakala, wati cholinga cha […]
The post Bushiri wasayinira mgwirizano ndi katsiwiri wa ma filimu Nkem Owoh wa dziko la Nigeria appeared first on Malawi 24.