Mneneri Shepherd Bushiri yemwe ndi mtsogoleri wa mpingo wa ECG – Jesus Nation Church walengeza kuti akufuna kugula ndege yonyamula anthu obwera ku mapemphero ake kuchokera m’mayiko ena. Izi ndi malingana ndi zomwe mneneriyu walemba pa tsamba lake la fesibuku lero Lachitatu pomwe wati lingaliroli labwera kamba koti akuona kuti ma kampani a ndege akumudyera […]
The post Bushiri walengeza zogula ndege appeared first on Malawi 24.